Radio Maria Malawi

Ulaliki wa Ulemelero wa Pansi Pano_Bambo Joseph Kimu

Informações:

Synopsis

Bambo Joseph Kimu ndi Funghai Mutsinze kukambirana za zotsatira za ulaliki umene umalonjeza anthu ulemelero wa pompopompo kapena kuti Gospel of Prosperity.